Acts 7:54 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene abwalo aja adamva mau a Stefanowo, adakwiya kwabasi, namchitira tsinya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pakumva izi analaswa mtima, namkukutira mano.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atamva zimenezi, iwo anakwiya kwambiri ndipo anamukukutira mano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pakumva izi analaswa mtima, namkukutira mano.