Acts 7:57 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma iwo adafuula kwambiri, natseka m'makutu mwao, namgudukira onse pamodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anafuula ndi mau akulu, natseka m'makutu mwao, namgumukira iye ndi mtima umodzi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma iwo anatseka mʼmakutu mwawo, ndipo anafuwula kolimba, onse anathamangira kwa iye,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anapfuula ndi mau akuru, natseka m'makutu mwao, namgumukira iye ndi mtima umodzi;