Acts 7:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Tsono makolo athuwo adachita nsanje ndi mbale wao Yosefe, ndipo adamgulitsa kuti akakhale kapolo ku Ejipito. Koma Mulungu anali naye,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo makolo akuluwa podukidwa naye Yosefe, anamgulitsa amuke naye ku Ejipito; ndipo Mulungu anali naye,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Makolo athu anachita nsanje ndi Yosefe ndipo anamugulitsa kuti akakhale kapolo ku Igupto. Koma Mulungu anali naye
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo makolo akuluwa podukidwa naye Yosefe, anamgulitsa amuke naye ku Aigupto; ndipo Mulungu anali naye,