Acts 8:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankamutsata chifukwa pa nthaŵi yaitali ankaŵadodometsa ndi matsenga akewo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamsamalira iye, popeza nthawi yaikulu adawadabwitsa iwo ndi matsenga ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu amamutsata chifukwa kwa nthawi yayitali amawadabwitsa ndi matsenga akewo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamsamalira iye, popeza nthawi yaikuru adawadabwitsa iwo ndi matsenga ace.