Acts 8:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti ndakuwona kuti ndiwe wodzaza ndi ndulu yoŵaŵa, ndiponso ndiwe womangidwa ndi maunyolo a zoipa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndiona kuti wagwidwa ndi ndulu yowawa ndi nsinga ya chosalungama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ine ndikuona kuti ndiwe wowawidwa mtima ndiponso kapolo wa tchimo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndiona kuti wagwidwa ndi ndulu yowawa ndi nsinga ya cosalungama.