Acts 8:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Filipo adatsikira ku mzinda wa ku Samariya, namalalikira anthu akumeneko za Khristu, Mpulumutsi wolonjezedwa uja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Filipo anatsikira kumudzi wa ku Samariya, nawalalikira iwo Khristu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Filipo anapita ku mzinda wa ku Samariya ndipo analalikira za Khristu kumeneko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Filipo anatsikira ku mudzi wa ku Samarlya, nawalalikira iwo Kristu.