Acts 9:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo waona m'masomphenya munthu wina, dzina lake Ananiya, akuloŵa ndi kumsanjika manja kuti apenyenso.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo anaona mwamuna dzina lake Ananiya, alikulowa, namuika manja, kuti apenyenso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo waona mʼmasomphenya munthu, dzina lake Hananiya atabwera ndi kumusanjika manja kuti aonenso.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo anaona mwamuna dzina, lace Hananiya, alikulowa, namuika manja, kuti apenyenso.