Acts 9:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo wabwera kuno ndi ulamuliro wa akulu a ansembe kuti adzamange onse otama dzina lanu mopemba.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kuti pano ali nao ulamuliro wa kwa ansembe aakulu wakumanga onse akuitana pa dzina lanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo wabwera kuno ndi ulamuliro wa akulu ansembe kuti adzamange onse amene amayitana pa dzina lanu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kuti pane ali nao ulamuliro wa kwa ansembe akulu wakumanga onse akuitana pa dzina lanu.