Acts 9:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo atadya chakudya, adapezanso mphamvu. Saulo adakhala masiku angapo limodzi ndi ophunzira a ku Damasiko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo analandira chakudya, naona nacho mphamvu. Ndipo anakhala pamodzi ndi ophunzira a ku Damasiko masiku ena.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo atadya chakudya, anapezanso mphamvu. Saulo anakhala masiku angapo ndi ophunzira a ku Damasiko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo ananyamuka nabatizidwa; ndipo analandira cakudya, naona naco mphamvu. Ndipo anakhala pamodzi ndi akuphunzira a ku Damasiko masiku ena.