Acts 9:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mphamvu za Saulo zinkakulirakulira, ndipo adathetsa nzeru Ayuda okhala ku Damasiko pakuŵatsimikizira kuti Yesu ndiyedi Mpulumutsi wolonjezedwa uja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Saulo anakula makamaka mumphamvu, nadodometsa Ayuda akukhala m'Damasiko, nawatsimikizira kuti ameneyo ndi Khristu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mphamvu za Saulo zinali kukulirakulira ndipo anathetsa nzeru Ayuda okhala ku Damasiko powatsimikizira kuti Yesu ndi Mpulumutsi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Saulo anakula makamaka mumphamvu, nadodometsa Ayuda akukhala m'Damasiko, nawatsimikizira kuti ameneyo ndi Kristu.