Acts 9:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ali paulendo wakewo, adayandikira mzinda wa Damasiko uja. Mwadzidzidzi kuŵala kochokera kumwamba kudamzinga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo poyenda ulendo wake, kunali kuti iye anayandikira Damasiko: ndipo mwadzidzidzi kudawala momzingira kuunika kochokera kumwamba;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akuyandikira ku Damasikoku paulendo wake, mwadzidzidzi kuwala kochokera kumwamba kunamuzungulira iye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo poyenda ulendo wace, kunali kuti iye anayandikira Damasiko: ndipo mwadzidzidzi kudawala momzingira kuunika kocokera kumwamba;