Acts 9:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene abale adamva zimenezi, adapita naye ku Kesareya namtumiza ku Tariso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma m'mene abale anachidziwa, anapita naye ku Kesareya, namtumiza achokeko kunka ku Tariso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abale atadziwa zimenezi, anamutenga Saulo ndi kupita naye ku Kaisareya, ndipo anamutumiza ku Tarisisi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma m'mene abale anacidziwa, anapita naye ku Kaisareya, namtumiza acokeko kunka ku Tariso.