Acts 9:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumeneko adapezako munthu wina, dzina lake Eneya, amene anali atagona pa mphasa zaka zisanu ndi zitatu, ali wofa ziwalo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapeza kumeneko munthu dzina lake Eneya, amene anagonera pamphasa zaka zisanu ndi zitatu; amene anagwidwa manjenje.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kumeneko anakapeza munthu dzina lake Eneya, wofa ziwalo amene anagona pa mphasa kwa zaka zisanu ndi zitatu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapeza kumeneko munthu dzina lace Eneya, amene anagonera pamphasa zaka zisanu ndi zitatu; amene anagwidwa manjenje.