Amos 2:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo ndine ndidasankha ena mwa ana anu kuti akhale aneneri, nkusankha ena mwa anyamata anu kuti akhale Anaziri. Kodi si choncho, inu anthu a ku Israele?” Akuterotu Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinaukitsa mwa ana anu aneneri, ndi mwa anyamata anu Anaziri. Si momwemo, inu ana a Israele, ati Yehova?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndinawutsanso ena mwa ana ako kuti akhale aneneri, ndi ena mwa anyamata ako kuti akhale anaziri. Kodi si choncho, inu Aisraeli?” akutero Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinaukitsa mwa ana anu aneneri, ndi mwa anyamata anu Anaziri. Si momwemo, inu ana a Israyeli, ati Yehova?