Amos 2:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mverani, ndidzakukanikizani pansi kwanuko, ndipo mudzalira ngati ngolo yodzaza ndi katundu wopitirira muyeso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, ndidzakupsinjani m'malo mwanu, monga lipsinja galeta lodzala ndi mitolo fwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsono Ine ndidzakupsinjani monga imapsinjikira ngolo imene yadzaza ndi tirigu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, ndidzakupsinjani m'malo mwanu, monga lipsinja gareta lodzala ndi mitolo fwa.