Amos 2:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wamauta sadzalimbika. Wothamanga sadzapulumuka, ndipo wokwera pa kavalo sadzapulumutsa moyo wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi wokoka uta sadzalimbika, ndi waliwiro sadzadzipulumutsa; ngakhale woyenda pa akavalo sadzapulumutsa moyo wake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wa uta sadzalimbika, msilikali wothamanga kwambiri sadzapulumuka, ndipo wokwera pa akavalo sadzapulumutsa moyo wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi wokoka uta sadzalimbika, ndi waliwiro sadzadzipulumutsa; ngakhale woyenda pa akavalo sadzapulumutsa moyo wace;