Amos 2:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa tsiku limenelo ngakhale wolimba mtima pakati pa anthu a mphamvu, adzathaŵa ali maliseche.” Akuterotu Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi wolimba mtima mwa ngwazi adzathawa wamaliseche tsiku lomwelo, ati Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale asilikali olimba mtima kwambiri adzathawa ali maliseche pa tsikulo,” akutero Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi wolimba mtima mwa ngwazi adzathawa wamarisece tsiku lomwelo, ati Yehova.