Amos 3:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ine ndidasankha ndi kusamala inu nokha pakati pa mitundu yonse ya pa dziko lapansi. Tsono ndidzakulangani koposa chifukwa cha machimo anu onse.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inu nokha ndinakudziwani mwa mabanja onse a pa dziko lapansi, m'mwemo ndidzakulangani chifukwa cha mphulupulu zanu zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Inu nokha ndi amene ndinakusankhani pakati pa mabanja onse a dziko lapansi; nʼchifukwa chake ndidzakulangani chifukwa cha machimo anu onse.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inu nokha ndinakudziwani mwa mabanja onse a pa dziko lapansi, m'mwemo ndidzakulangani cifukwa ca mphulupulu zanu zonse.