Amos 4:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ambuye Chauta, ndi kuyera kwao kuja, alumbira kuti, “Pali Ine ndemwe, masiku a chilango chanu akudza ndithu! Nthaŵiyo anthu adzakuguguzani ndi ngoŵe. Adzakukokani ndi mbedza nonse mpaka wotsiriza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ambuye Yehova walumbira pali chiyero chake, kuti taonani, adzakugwerani masiku akuti adzakuchotsani ndi zokowera, ndi otsala anu ndi mbedza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ambuye Yehova, mwa kuyera mtima kwake walumbira kuti, “Nthawi idzafika ndithu pamene adzakukokani ndi ngowe, womaliza wa inu adzakokedwa ndi mbedza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ambuye Yehova walumbira pali ciyero cace, kuti taonani, adzakugwerani masiku akuti adzakucotsani ndi zokowera, ndi otsala anu ndi mbedza.