Amos 4:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mupereke buledi wanu kuti muthokoze Mulungu. Munene poyera ndi kulengeza zopereka zanu zaufulu, pakuti nzimene mumakonda kuchita, inu Aisraele.” Akutero Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nimutenthe nsembe zolemekeza zachotupitsa, nimulalikire nsembe zaufulu, ndi kuzimveketsa; pakuti ichi muchikonda, inu ana a Israele, ati Ambuye Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wotchani buledi wokhala ndi yisiti ngati nsembe yachiyamiko ndi kumanyadira poyera za zopereka zanu zaufulu. Inu Aisraeli, zinyadireni nsembezo, pakuti izi ndi zimene mumakonda kuchita,” akutero Ambuye Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nimutenthe nsembe zolemekeza zacotupitsa, nimulalikire nsembe zaufulu, ndi kuzimveketsa; pakuti ici mucikonda, inu ana a Israyeli, ati Ambuye Yehova.