Amos 5:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu banja la Israele imvani mau aŵa, amene ndikukuuzani mwadandaulo:
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tamverani mau awa ndinenawa, akhalire inu nyimbo ya maliro, nyumba ya Israele inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Israeli, imva mawu awa, nyimbo ya maliro imene ndikuyimba za iweyo:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tamverani mau awa ndinenawa, akhalire inu nyimbo ya maliro, nyumba ya Israyeli inu.