Amos 5:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mumadana ndi muweruzi wodzudzula zosalungama, mumanyansidwa ndi wokamba zoona pa bwalo lamilandu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo adana naye wodzudzula kuchipata, nanyansidwa naye wolunjikitsa mau.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
inu mumadana ndi amene amadzudzula mʼbwalo la milandu ndi kunyoza amene amanena zoona.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo adana naye wodzudzula kucipata, nanyansidwa naye wolunjikitsa mau.