Amos 5:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Namwali Israele wagwa chonse osati nkudzukanso ai. Wagwa ndi kuiŵalika pa dziko lake, popanda wina womdzutsa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Namwali wa Israele wagwa, sadzaukanso; wagwetsedwa pa nthaka yake, palibe womuutsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Namwali Israeli wagwa, moti sadzadzukanso, wasiyidwa mʼdziko lake lomwe, popanda woti ndi kumudzutsa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Namwali wa Israyeli wagwa, sadzaukanso; wagwetsedwa pa nthaka yace, palibe womuutsa.