Amos 5:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma kuweruza kwanu kwangwiro kuziyenda kosalekeza ngati madzi, kulungama kwanu kukhale ngati mtsinje wosaphwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma chiweruzo chiyende ngati madzi, ndi chilungamo ngati mtsinje wosefuka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma chiweruzo cholungama chiyende ngati madzi, chilungamo ngati mtsinje wosaphwa!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ciweruzo ciyende ngati madzi, ndi cilungamo ngati mtsinje wosefuka.