Amos 5:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Kodi inu anthu a ku Israele, zaka makumi anai zimene mudakhala m'chipululu, mudanditsirirako nsembe ndi kundipatsa mitulo?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati munabwera nazo kwa Ine nsembe zophera ndi zaufa zaka makumi anai m'chipululu, inu nyumba ya Israele?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kodi pa zaka makumi anayi zimene munakhala mʼchipululu muja munkandibweretsera nsembe ndi zopereka, inu nyumba ya Israeli?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati munabwera nazo kwa Ine nsembe zophera ndi zaufa zaka makumi anai m'cipululu, inu nyumba ya Israyeli?