Amos 5:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipotu muzidzanyamula Sakuti, mfumu yanu, ndi nyenyezi ija Kaiwani, mulungu wanu, mafano amene mudadzipangira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inde mwasenza hema wa mfumu yanu, ndi tsinde la mafano anu, nyenyezi ya mulungu wanu, amene mudadzipangira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mwanyamula kachisi wa mfumu yanu, ndi nyenyezi ija Kaiwani, mulungu wanu, mafano amene munadzipangira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inde mwasenza hema wa mfumu yanu, ndi tsinde la mafano anu, nyenyezi ya mlungu wanu, amene mudadzipangira.