Amos 5:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti ndidzakupititsani ku ukapolo, kutali kupitirira mzinda wa Damasiko.” Akutero Chauta, amene dzina lake ndi Mulungu Wamphamvuzonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'mwemo ndidzakutengani kunka nanu kundende kutsogolo kwa Damasiko, ati Yehova, amene dzina lake ndiye Mulungu wa makamu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake Ine ndidzakupititsani ku ukapolo, kutali kupitirira ku Damasiko,” akutero Yehova, amene dzina lake ndi Mulungu Wamphamvuzonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'mwemo ndidzakutengani kumka nanu kundende kutsogolo kwa Damasiko, ati Yehova, amene dzina lace ndiye Mulungu wa makamu.