Amos 5:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiyenso amene amakantha olamulira ankhanza, ndiye amene amagumula malinga ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
wakufikitsa chionongeko pa wamphamvu modzidzimuka, chionongeko nichigwera linga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iyeyo amabweretsa chiwonongeko modzidzimutsa pa anthu amphamvu ndi kuwononga mizinda yotetezedwa),
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
wakufikitsa cionongeko pa wamphamvu modzidzimuka, cionongeko nicigwera linga,