Amos 6:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu simulabadako zoti kudzafika tsiku lachilango, zochita zanu zimafulumizitsa nthaŵi yachiwawayo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inu akutalikitsa tsiku loipa, ndi kusendeza pafupi mpando wachiwawa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu simulabadirako kuti tsiku loyipa lidzafika, zochita zanu zimafulumizitsa ulamuliro wankhanza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inu akutalikitsa tsiku loipa, ndi kusendeza pafupi mpando waciwawa;