Amos 6:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ntchito nkumangoimba azeze ngati Davide, ndi kumangopeka nyimbo zoimbira pa zing'wenyeng'wenye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
akungoimba kutsata maliridwe a zeze, nadzilingiririra zoimbira nazo ngati Davide;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mumayimba azeze anu ndi kumangopeka nyimbo pa zingʼwenyengʼwenye ngati Davide.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
akungoyimba kutsata maliridwe a zeze, nadzilingiririra zoyimbira nazo Ingati Davide;