Amos 6:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu khumi akadzakhala akubisala m'nyumba imodzi, nawonso adzafabe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kudzachitika, mukatsala amuna khumi m'nyumba imodzi, adzafa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati anthu khumi otsala adzabisala mʼnyumba imodzi, nawonso adzafa ndithu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kudzacitika, mukatsala amuna khumi m'nyumba imodzi, adzafa.