Amos 7:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Amosiyo akunena kuti, ‘Yerobowamu adzafa pa nkhondo, ndipo Aisraele adzatengedwa kunka ku ukapolo, kutali ndi dziko lao.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti atero Amosi, Yerobowamu adzafa ndi lupanga, ndi Israele adzatengedwadi ndende, kuchoka m'dziko lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti zimene Amosi akunena ndi izi: “ ‘Yeroboamu adzaphedwa ndi lupanga, ndipo Israeli adzapita ndithu ku ukapolo, kutali ndi dziko lake.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti atero Amosi, Yerobiamu adzafa ndi lupanga, ndi Israyeli adzatengedwadi ndende, kucoka m'dziko lace.