Amos 7:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma usakalosenso ku Betele poti kumeneko ndi malo opatulika a mfumu, ndiponso ndi Nyumba ya Mulungu ya m'dziko lino.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma usaneneranso ku Betele; pakuti pamenepo mpa malo opatulika a mfumu, ndiyo nyumba yachifumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Usanenerenso ku Beteli, chifukwa kumeneko ndi malo opatulika a mfumu ndiponso ndi malo a nyumba yachipembedzo yaufumu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma usaneneranso ku Beteli; pakuti pamenepo mpa malo opatulika a mfumu, ndiyo nyumba yacifumu.