Amos 7:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ine ndidati, “Inu Ambuye Chauta, ndapota nanu, basi lekani. Kodi anthu a Yakobeŵa angalimbike bwanji? Iwoŵa ndi ofooka kwambiri.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo ndinati, Ambuye Yehova, lekanitu; Yakobo adzakhala chilili bwanji? Pakuti ali wamng'ono.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono ine ndinafuwula kuti, “Ambuye Yehova, chonde ndikukupemphani, lekani! Kodi Yakobo adzapulumuka bwanji? Iye ndi wofowoka kwambiri!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo ndinati, Ambuye Yehova, Iekanitu; Yakobo adzakhala ciriri bwanji? pakuti ali wamng'ono.