Amos 8:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amosi adati, “Imvani izi, inu amene mumapondereza osoŵa, amene mufuna kuwononga anthu osauka am'dzikomu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tamverani ichi, inu akumeza aumphawi, ndi kuwatha ofatsa m'dziko, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Imvani izi, inu amene mumapondereza anthu osowa ndipo simulabadira anthu osauka a mʼdzikomu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tamverani ici, inu akumeza aumphawi, ndi kuwatha ofatsa m'dziko, ndi kuti,