Amos 8:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuti osauka tiŵagule ndi siliva, amphaŵi tiŵagule ndi nkhwaŵiro, kutinso tigulitse ndi mungu womwe wa tirigu?’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti tigule osauka ndi ndalama, ndi aumphawi ndi nsapato, ndi kugulitsa nsadwa za tirigu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
tigule osauka ndi ndalama zasiliva ndi osowa powapatsa nsapato, tigulitse ngakhale mungu wa tirigu?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti tigule osauka ndi ndarama, ndi aumphawi ndi nsapato, ndi kugulitsa nsadwa za tirigu.