Amos 8:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ambuye Chauta akunena kuti, “Pa tsiku limenelo ndidzadetsa dzuŵa masana, ndidzagwetsa mdima pa dziko lapansi dzuŵa lili nye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kudzachitika tsiku lomwelo, ati Ambuye Yehova, ndidzalowetsa dzuwa usana, ndi kudetsa dziko pausana poyera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsiku limenelo,” Ambuye Yehova akunena kuti, “Ndidzadetsa dzuwa masana ndi kugwetsa mdima pa dziko lapansi dzuwa likuswa mtengo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kudzacitika tsiku lomwelo, ati Ambuye Yehova, ndidzalowetsa dzuwa usana, ndi kudetsa dziko pausana poyera.