Amos 9:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzafera pa nkhondo anthu anga onse ochimwa, iwo amene amati, ‘Chilango sichidzatifika, kapena kutipambana.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ochimwa onse a anthu anga adzafa ndi lupanga, ndiwo amene akuti, Choipa sichidzatipeza, kapena kutidulira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu onse ochimwa pakati pa anthu anga adzaphedwa ndi lupanga, onse amene amanena kuti, ‘Tsoka silidzatigwera ife kapena kutiwononga.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ocimwa onse a anthu anga adzafa ndi lupanga, ndiwo amene akuti, Coipa sicidzatipeza, kapena kutidulira.