Amos 9:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi imeneyo Aisraele otsala adzagonjetsa zimene zatsala za ku Edomu, pamodzi ndi maiko onse amene amadziŵika ndi dzina langa.” Akuterotu Chauta, amene adzachitedi zimene wanenazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti alandire otsala a Edomu akhale cholowa chao, ndi amitundu onse a kutchedwa dzina langa, ati Yehova wakuchita izi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti adzatengenso otsala a Edomu ndi mitundu yonse imene imatchedwa ndi dzina langa,” akutero Yehova amene adzachita zinthu izi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti alandire otsala a Edomu akhale colowa cao, ndi amitundu onse akuchedwa dzina langa, ati Yehova wakucita izi.