Colossians 1:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kale inu munali kutali ndi Mulungu, ndipo munkadana naye m'maganizo anu ndi m'ntchito zanu zoipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo inu, okhala alendo kale ndi adani m'chifuwa chanu m'ntchito zoipazo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kale inu munali kutali ndi Mulungu ndipo munali adani a Mulungu mʼmaganizo mwanu chifukwa cha khalidwe lanu loyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo inu, okhala alendo kale ndi adani m'cifuwa canu m'nchito zoipazo, koma tsopano anakuyanjanitsani