Colossians 1:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Gwero la zonsezi ndi chiyembekezo chimene muli nacho chodzalandira zimene Mulungu akukusungirani Kumwamba. Mudamva za zimenezi pamene mau oona, adakufikani poyamba paja. Mau oonawo ndi Uthenga Wabwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa cha chiyembekezo chosungikira kwa inu m'Mwamba, chimene mudachimva kale m'mau a choonadi cha Uthenga Wabwino,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chikhulupiriro ndi chikondi, gwero lake ndi chiyembekezo chomwe muli nacho chodzalandira zimene anakusungirani kumwamba. Munamva kale za zimenezi kudzera mʼmawu a choonadi, Uthenga Wabwino
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cifukwa ca ciyembekezo cosungikira kwa inu m'Mwamba, cimene mudacimva kale m'mau a coonadi ca Uthenga Wabwino,