Colossians 2:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Malamulo ameneŵa ndi zophunzitsa zimenezi ndi za anthu chabe, ndipo zimangokhudza zinthu zimene zimatha, anthu akamazigwiritsa ntchito.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
(ndizo zonse zakuonongedwa pochita nazo), monga mwa malangizo ndi maphunziro a anthu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Malamulo amenewa amakhudza zinthu zimene zimatha zikamagwiritsidwa ntchito, ndipo malamulo ndi zophunzitsa za anthu chabe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
(ndizo zonse zakuonongedwa pocita nazo), monga mwa malangizo ndi maphunziro a anthu?