Colossians 2:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kwinaku mauwo amaoneka ngati anzeru, pakuti amalamula anthu zambiri pa za kupembedza, za kudzichepetsa ndi za kuzunza thupi lao. Komabe malamulowo alibe phindu, ndipo sathandiza konse kugonjetsa khalidwe longosangalatsa thupi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zimene zili naotu manenedwe a nzeru m'kutumikira kwa chifuniro cha mwini wake, ndi kudzichepetsa, ndi kusalabadira thupi; koma zilibe mphamvu konse yakuletsa chikhutitso cha thupi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndithu malamulo oterewa amaoneka ngati anzeru, pakuti amalamulira anthu ambiri pa zachipembedzo ndi pa zakudzichepetsa kwa chiphamaso, ndi pa zakuzunza thupi lawo, koma alibe mphamvu zoletsa kuchita zofuna za thupilo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
zimene ziri naotu manenedwe a nzeru m'kutumikira kwa cifuniro ca mwini wace, ndi kudzicepetsa, ndi kusalabadira thupi; koma ziribe mphamvu konse yakuletsa cikhutitso ca thupi.