Colossians 2:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikunenatu zimenezi, kuwopa kuti wina aliyense angakukopeni ndi mau onyenga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ichi ndinena, kuti munthu asakusokeretseni inu ndi mau okopakopa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikukuwuzani zimenezi kuti wina aliyense asakunamizeni ndi kukukopani ndi mawu ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ici ndinena, kuti munthu asakusokeretseni inu ndi mau okopakopa.