Colossians 3:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja mukudziŵa kuti Ambuye adzakupatsani mphotho. Mphothoyo ndi madalitso amene adalonjeza kudzapatsa anthu ake. Ambuye amene mukuŵatumikirawo ndi Khristu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
podziwa kuti mudzalandira kwa Ambuye mphotho ya cholowa; mutumikira Ambuye Khristu mwaukapolo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mukudziwa kuti mudzalandira mphotho monga cholowa kuchokera kwa Ambuye. Ndi Ambuye Khristu amene mukumutumikira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
podziwa kuti mudzalandira kwa Ambuye mphotho ya colowa; mutumikira Ambuye Kristu mwaukapolo.