Colossians 3:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma munthu amene amachita zosalungama, zidzamubwerera, chifukwa Mulungu amaweruza mosakondera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti iye wakuchita chosalungama adzalandiranso chosalungama anachitacho; ndipo palibe tsankho.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aliyense amene amachita zolakwa adzalandira malipiro molingana ndi kulakwa kwake, ndipo palibe tsankho.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti iye wakucita cosalungama adzalandiranso cosalungama anaeitaco; ndipo 1 palibe tsankhu.