Colossians 3:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa cha zinthu zotere Mulungu amaŵakwiyira anthu osamumvera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa cha izi zomwe ukudza mkwiyo wa Mulungu pa ana a kusamvera;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa cha zimenezi, mkwiyo wa Mulungu ukubwera pa ana osamvera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cifukwa ca izi zomwe ukudza mkwiyo wa Mulungu pa ana a kusamvera;