Colossians 4:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mutiperekereko moni kwa abale athu okhala ku Laodikea, ndiponso kwa Nimfa ndi kwa ampingo amene amasonkhana kunyumba kwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akupatsani moni abalewo a m'Laodikea, ndi Nimfa, ndi Mpingowo wa m'nyumba yao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Perekani moni kwa abale a ku Laodikaya, ndiponso kwa Numfa ndi mpingo wa mʼnyumba mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Lankhulani abalewo a m'Laodikaya, ndi Numfa, ndi Mpingowo wa m'nyumba yao.