Colossians 4:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mayendedwe anu pakati pa anthu akunja azikhala anzeru, ndipo muzichita changu, osataya nthaŵi pachabe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muyendere munzeru ndi iwo akunja, kuchita machawi nthawi ingatayike.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mayendedwe anu pakati pa akunja, akhale anzeru ndipo mugwiritse ntchito mpata uliwonse umene muli nawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muyendere munzeru ndi iwo akunja, kucita macawi nthawi ingatayike.