Daniel 1:11 — Compare Translations
3 translations compared side by side
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati Daniele kwa kapitao, amene mkulu wa adindo adamuikayo ayang'anire Daniele, Hananiya, Misaele, ndi Azariya,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Danieli anati kwa kapitawo amene anali mkulu wa nduna za mfumu amene anamuyika kuti ayangʼanire Danieli, Hananiya, Misaeli ndi Azariya,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati Danieli kwa kapitao, amene mkuru wa adindo adamuikayo ayang'anire Danieli, Hananiya, Misaeli, ndi Azariya,